[Music Download]Aubkay – Fanana

 [Music Download]Aubkay – Fanana
Aubkay – Fanana
Aubkay – Fanana

Heyiye
Its your boy Aubkay
Ghetto pride Entertainment
_
Hele helelemama

Verse1

Zintchito zanga
Zokamba zanga
Zifanane nanu yesu
Its my prayer day & Night
Musalore phazi langa litereleke
Everything I do
Should please you
Everything I do
Should please you God

Chorus
Fanana ndizifanana
Fanana nanu yesu
Ndikamayenda (Fanana
Ndikamakhala (fanana)
Fanana nanu yesu

Verse 2

Ndinu achifundo
Ndinu achikondi
Mumachiza zinthenda
Mumatonthoza olira
Masana utsiku
Inshort you are the God of possible things
There’s nothing which is impossible with you

Size: 8 MB