The Three Chingas: Steve, Miracle and Israel Collaborate in Wauka

 The Three Chingas: Steve, Miracle and Israel Collaborate in Wauka

By Mercy Maulana,

Just right on time. Easter time:celebrating the crucifixion, death and resurrection of our Lord Jesus Christ, The Chingas have released Wauka meaning ‘He is risen’.

[Music Download] Steve Spesho – Wauka Ft Miracle Chinga and Israel Chinga

Speaking to zambuye.com, Steve Spesho said that the three thought of sharing something to celebrate the death and resurrection of Jesus Christ.

He said, “Its a celebration song that Jesus Christ defeated death and e is risen!”

In a separate Interview, Miracle said,
She said “Its a celebration song, the death of Jesus brought us salvation and many benefits and His resurrection is worthy cerebrating.”

Song: Wauka
Artist: Steve Spesho Feat. Miracle Chinga, Israel Chinga-Moffat
Album: Grace
written: by Steve Spesho, Miracle Chinga, Israel Chinga-Moffat

(Verse 1) By Steve Spesho

Poti yehovah ana konda dzikoli,
Ana tuma mwana wake
wobadwa yekha/
Kuti yense omu khulupilira asatayike
akhale ndi moyo osatha/

Anatifela pa mtanda yesu, aaah yesu
kutiombola ife yes, aaah yes
ananena kale kuti adzauka iye
apa si izi waukadi iye/

ana pita ku hade konko kukamulanda makiyi mdyelekezi,
kugonjetsa imfa, nkudzuka popanda otsutsa,
machimo anthu atatsuka/

mmanda mulibemo umo, mmanda mulibemo umo,
chimwala chasunthidwa.. aaah..
mufuniranji munthu wa moyo
pakati pa anthu akufa?

(Chorus)
wauka yesu wauka,
wauka yesu wauka,
wauka yesu wauka,
wauka yesu wauka,

wauka yesu wauka,
Tamvetsetsani zomwe nkunenazi,
wauka yesu wauka,
mmanda mulibemo umo,
wauka yesu wauka,
tamvetsetsani zomwe nkunenazi
wauka yesu wauka,
Chipulumutso chatheka..

(Verse 2) By Miracle Chinga

Chimwala cha phathiphathi chija,
chasunthidwa, pamanda paja palibe,
-wauka eeh wauka eeh
petulo wangopezapo nsalu za maliro zokha zokha
koma mwana wa mulungu kulibe
-wauka eeh wauka eeh
Atumwi nawo aku kaika,
azimayi sakukhulupiliranso
kulibe
-wauka eeh wauka eeh
mosanama mosabisa
waukira ife tonse
anafela machimo anthu tikondwele
timlandile
halleluya.

(Chorus)
wauka yesu wauka,
wauka yesu wauka,
wauka yesu wauka,
wauka yesu wauka,

wauka yesu wauka,
Tamvetsetsani zomwe nkunenazi,
wauka yesu wauka,
mmanda mulibemo umo,
wauka yesu wauka,
tamvetsetsani zomwe nkunenazi
wauka yesu wauka,
Chipulumutso chatheka..

Verse By Israel Chinga Moffat

Kodi mwamva?
mwana wa yosefe ku manda kulibe,
odi mwamva?
mwana wa yosefe kumanda kulibe eeh

anapitako maliya,
wapeza yesu kulibe..
anapitako maliya,
wapeza yesu kulibe..

koma ine i remember
ananena tsiku ngati lero adzauka
koma ine i remember
adakamba tsiku ngati la lero adzauka

wauka, wauka
sindikukaikira eeeh,
wauka, wauka
sindikukaikira eya

(Chorus)
wauka yesu wauka,
wauka yesu wauka,
wauka yesu wauka,
wauka yesu wauka,

wauka yesu wauka,
Tamvetsetsani zomwe nkunenazi,
wauka yesu wauka,
mmanda mulibemo umo,
wauka yesu wauka,
tamvetsetsani zomwe nkunenazi
wauka yesu wauka,
Chipulumutso chatheka.